Luka 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma atangofika mwana wanuyu, amene anawononga* chuma chanu ndi mahule, mwamuphera mwana wa ngʼombe wamphongo wonenepa bwino.’ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:30 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 202-203 Nsanja ya Olonda,10/1/1998, ptsa. 14-16
30 Koma atangofika mwana wanuyu, amene anawononga* chuma chanu ndi mahule, mwamuphera mwana wa ngʼombe wamphongo wonenepa bwino.’