-
Luka 15:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Bambo akewo anamuuza kuti, ‘Mwana wanga, iwe wakhala nane nthawi zonse ndipo zinthu zonse zimene ine ndili nazo ndi zako.
-