-
Luka 15:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Komatu tinangoyenera kusangalala ndi kukondwera, chifukwa mʼbale wakoyu anali wakufa koma panopa ali ndi moyo, anatayika koma panopa wapezeka.’”
-