-
Luka 16:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako anauzanso ophunzira ake kuti: “Munthu wina wolemera anali ndi mtumiki woyangʼanira nyumba yake, amene anthu ena anamuneneza kuti akumusakazira chuma.
-