-
Luka 16:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho anamuitana nʼkumuuza kuti, ‘Ndamva zoipa zimene ukuchita. Pita ukalembe lipoti la mmene wakhala ukugwirira ntchito yoyangʼanira nyumba ino nʼkundipatsa, chifukwa supitiriza kuyendetsa ntchito zapanyumba pano.’
-