-
Luka 16:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno mtumikiyo mumtima mwake anati, ‘Nditani ine? Abwana anga akufuna kundichotsa ntchito. Sindingathe kulima chifukwa ndilibe mphamvu ndipo ndikuchita manyazi kuti ndikhale wopemphapempha.
-