-
Luka 16:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno anaitana amene anali ndi ngongole kwa bwana wake mmodzi ndi mmodzi, ndipo anafunsa woyamba kuti, ‘Uli ndi ngongole yochuluka bwanji kwa bwana wanga?’
-