Luka 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anafunsa wina kuti, ‘Nanga iwe, ngongole yako ndi yochuluka bwanji?’ Iye anayankha kuti, ‘Madengu 100 a tirigu.’* Iye anamuuza kuti, ‘Tenga kalata ya mgwirizano wa ngongole yako ndipo ulembepo madengu 80.’ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 204 Nsanja ya Olonda,3/1/1989, tsa. 8
7 Kenako anafunsa wina kuti, ‘Nanga iwe, ngongole yako ndi yochuluka bwanji?’ Iye anayankha kuti, ‘Madengu 100 a tirigu.’* Iye anamuuza kuti, ‘Tenga kalata ya mgwirizano wa ngongole yako ndipo ulembepo madengu 80.’