Luka 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Bwana wake uja anayamikira mtumiki ameneyu, ngakhale kuti anali wosalungama, chifukwa anachita zinthu mwanzeru.* Chifukwa ana a mu nthawi ino* amachita mwanzeru akamachita zinthu ndi anthu a mʼbadwo wawo kuposa ana a kuwala.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:8 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 204-205 Nsanja ya Olonda,3/1/1989, ptsa. 8-9
8 Bwana wake uja anayamikira mtumiki ameneyu, ngakhale kuti anali wosalungama, chifukwa anachita zinthu mwanzeru.* Chifukwa ana a mu nthawi ino* amachita mwanzeru akamachita zinthu ndi anthu a mʼbadwo wawo kuposa ana a kuwala.+