Luka 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mtumiki sangakhale kapolo wa ambuye awiri, chifukwa akhoza kudana ndi mmodzi nʼkukonda winayo, kapena angakhale wokhulupirika kwa mmodzi nʼkunyoza winayo. Simungakhale akapolo a Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:13 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 46
13 Mtumiki sangakhale kapolo wa ambuye awiri, chifukwa akhoza kudana ndi mmodzi nʼkukonda winayo, kapena angakhale wokhulupirika kwa mmodzi nʼkunyoza winayo. Simungakhale akapolo a Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.”+