Luka 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Afarisi amene ankakonda kwambiri ndalama, ankamvetsera zonsezi ndipo anayamba kumunyoza.+