Luka 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho iye anawauza kuti: “Inu ndi amene mumanena pamaso pa anthu kuti ndinu olungama,+ koma Mulungu akudziwa mitima yanu.+ Chifukwa chimene anthu amachiona kuti ndi chapamwamba ndi chonyansa pamaso pa Mulungu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 206 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, ptsa. 12-13
15 Choncho iye anawauza kuti: “Inu ndi amene mumanena pamaso pa anthu kuti ndinu olungama,+ koma Mulungu akudziwa mitima yanu.+ Chifukwa chimene anthu amachiona kuti ndi chapamwamba ndi chonyansa pamaso pa Mulungu.+