Luka 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndithudi, nʼzosavuta kuti kumwamba ndi dziko lapansi zichoke kusiyana ndi kuti kachigawo kakangʼono ka chilembo cha mʼChilamulo kasakwaniritsidwe.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:17 Yesu—Ndi Njira, tsa. 206 Nsanja ya Olonda,6/1/1988, tsa. 30
17 Ndithudi, nʼzosavuta kuti kumwamba ndi dziko lapansi zichoke kusiyana ndi kuti kachigawo kakangʼono ka chilembo cha mʼChilamulo kasakwaniritsidwe.+