Luka 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina, wachita chigololo ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:18 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2018, ptsa. 11-12 Nsanja ya Olonda,3/15/1989, tsa. 8
18 Aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina, wachita chigololo ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+