-
Luka 16:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Komanso panali munthu wina wopemphapempha, amene anali ndi zilonda thupi lonse dzina lake Lazaro ndipo anthu ankamukhazika pageti la munthu wachumayo.
-