Luka 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi wopemphapempha uja anamwalira ndipo angelo anamutenga kukamuika pambali pa Abulahamu.* Munthu wachuma ujanso anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:22 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 208-209 Nsanja ya Olonda,4/1/1989, ptsa. 24-25
22 Patapita nthawi wopemphapempha uja anamwalira ndipo angelo anamutenga kukamuika pambali pa Abulahamu.* Munthu wachuma ujanso anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda.