-
Luka 16:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Choncho anaitana kuti, ‘Atate Abulahamu, ndichitireni chifundo. Mutume Lazaro kuti aviike nsonga ya chala chake mʼmadzi kuti aziziritse lilime langa, chifukwa ndikuzunzika mʼmoto wolilimawu.’
-