-
Luka 16:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Komanso pakati pa ife ndi inu paikidwa phompho lalikulu kwambiri, moti amene akufuna kubwera kumeneko kuchokera kuno sangathe. Komanso anthu sangaoloke kuchokera kumeneko kubwera kuno.’
-