Luka 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma iye anamuuza kuti, ‘Ngati sakumvera zolemba za Mose+ komanso za aneneri, sangathekebe ngakhale wina atauka kwa akufa.’” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:31 Nsanja ya Olonda,4/1/1989, tsa. 25
31 Koma iye anamuuza kuti, ‘Ngati sakumvera zolemba za Mose+ komanso za aneneri, sangathekebe ngakhale wina atauka kwa akufa.’”