Luka 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale atakuchimwira maulendo 7 pa tsiku, nʼkubwera kwa iwe maulendo 7 kudzanena kuti, ‘Ndalapa ine,’ umukhululukire ndithu.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:4 Yesu—Ndi Njira, tsa. 210 Galamukani!,8/8/1995, tsa. 10
4 Ngakhale atakuchimwira maulendo 7 pa tsiku, nʼkubwera kwa iwe maulendo 7 kudzanena kuti, ‘Ndalapa ine,’ umukhululukire ndithu.”+