Luka 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesu atawaona anawauza kuti: “Pitani mukadzionetse kwa ansembe.”+ Ndiyeno pamene ankapita anayeretsedwa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 216 Nsanja ya Olonda,6/1/1989, tsa. 8
14 Yesu atawaona anawauza kuti: “Pitani mukadzionetse kwa ansembe.”+ Ndiyeno pamene ankapita anayeretsedwa.+