-
Luka 17:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Masiku akubwera pamene mudzalakalaka kuona limodzi la masiku a Mwana wa munthu koma simudzaliona.
-