Luka 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse komanso kuti asamataye mtima.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 220 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 8
18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse komanso kuti asamataye mtima.+