-
Luka 18:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mumzindawo munalinso mkazi wamasiye amene ankapitapita kwa woweruza uja kukamupempha kuti, ‘Ndiweruzireni mlandu wanga ndi munthu amene ndili naye pa mlandu, kuti pachitike chilungamo.’
-