-
Luka 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kwa kanthawi ndithu woweruzayo sankafuna, koma pambuyo pake ananena mumtima mwake kuti, ‘Ngakhale kuti sindiopa Mulungu kapena kusamala za munthu aliyense,
-