Luka 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndionetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa mkazi wamasiyeyu chifukwa choti akundivutitsa. Ndichita zimenezi kuti asapitirize kubwera nʼkunditopetsa ndi zimene akupemphazo.’”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:5 Nsanja ya Olonda,4/1/2014, tsa. 7
5 ndionetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa mkazi wamasiyeyu chifukwa choti akundivutitsa. Ndichita zimenezi kuti asapitirize kubwera nʼkunditopetsa ndi zimene akupemphazo.’”+