-
Luka 18:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mfarisi uja anaimirira nʼkuyamba kupemphera mumtima mwake kuti, ‘Mulungu wanga, ndikukuyamikani chifukwa ndine wosiyana ndi anthu ena onse. Iwo ndi achifwamba, osalungama komanso achigololo. Ndinenso wosiyana ndi wokhometsa msonkho uyu.
-