Luka 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndithu ndikukuuzani, munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kuti ndi wolungama kwambiri kuposa Mfarisi uja.+ Chifukwa aliyense wodzikweza adzachititsidwa manyazi, koma aliyense amene amadzichepetsa adzakwezedwa.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 221 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 97/15/1987, tsa. 10
14 Ndithu ndikukuuzani, munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kuti ndi wolungama kwambiri kuposa Mfarisi uja.+ Chifukwa aliyense wodzikweza adzachititsidwa manyazi, koma aliyense amene amadzichepetsa adzakwezedwa.”+