22 Yesu atamva zimenezo, anamuuza kuti: “Pali chinthu chimodzi chimene chikusowekabe mwa iwe: Ukagulitse zinthu zonse zimene uli nazo ndipo ndalamazo ukagawe kwa anthu osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba, ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+