-
Luka 18:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Ndiyeno anthu amene anali patsogolo anayamba kumudzudzula nʼkumamuuza kuti akhale chete. Koma akatero mʼpamenenso iye ankafuula kwambiri kuti: “Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo!”
-