Luka 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Zakeyu anaimirira nʼkuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense* ndibweza kuwirikiza ka 4.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:8 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 230-231 Nsanja ya Olonda,9/15/1989, ptsa. 8-98/15/1989, tsa. 5
8 Koma Zakeyu anaimirira nʼkuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense* ndibweza kuwirikiza ka 4.”+