Luka 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene iwo ankamvetsera zimenezi, iye anawauza fanizo lina, chifukwa anali pafupi ndi Yerusalemu ndipo anthuwo ankaganiza kuti Ufumu wa Mulungu uonekera nthawi yomweyo.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:11 Yesu—Ndi Njira, tsa. 232 Nsanja ya Olonda,10/1/1989, tsa. 8
11 Pamene iwo ankamvetsera zimenezi, iye anawauza fanizo lina, chifukwa anali pafupi ndi Yerusalemu ndipo anthuwo ankaganiza kuti Ufumu wa Mulungu uonekera nthawi yomweyo.+