Luka 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndinachita zimenezi chifukwa ndimakuopani. Inutu ndinu munthu wouma mtima. Mumatenga zimene simunasungitse ndipo mumakolola zimene simunafese.’+
21 Ndinachita zimenezi chifukwa ndimakuopani. Inutu ndinu munthu wouma mtima. Mumatenga zimene simunasungitse ndipo mumakolola zimene simunafese.’+