Luka 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho anthu amene anatumidwawo ananyamuka ndipo anakamupezadi mmene iye anawauzira.+