Luka 19:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo tsiku ndi tsiku iye anapitiriza kuphunzitsa mʼkachisimo. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu ankafunitsitsa kumupha.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:47 Yesu—Ndi Njira, tsa. 240 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 8
47 Ndipo tsiku ndi tsiku iye anapitiriza kuphunzitsa mʼkachisimo. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu ankafunitsitsa kumupha.+