Luka 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 nʼkudzamufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndi ndani amene anakupatsani ulamuliro umenewu?”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 244 Nsanja ya Olonda,12/15/1989, tsa. 8
2 nʼkudzamufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndi ndani amene anakupatsani ulamuliro umenewu?”+