-
Luka 20:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho iwo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, tikudziwa kuti zimene mumanena ndi kuphunzitsa ndi zolondola ndipo mulibe tsankho, koma mumaphunzitsa njira ya Mulungu mogwirizana ndi choonadi.
-