Luka 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Ndionetseni khobidi la dinari.* Kodi nkhope ndi mawu ali pamenepo ndi za ndani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.”
24 “Ndionetseni khobidi la dinari.* Kodi nkhope ndi mawu ali pamenepo ndi za ndani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.”