-
Luka 20:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Iwo analephera kumutapa mʼkamwa pa zimene ananenazi pamaso pa anthu, koma anadabwa ndi yankho lake moti anangokhala chete kusowa chonena.
-