Luka 20:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma amene aonedwa kuti ndi oyenerera kudzapeza moyo pa nthawi imeneyo nʼkudzaukitsidwa kwa akufa sadzakwatira kapena kukwatiwa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:35 Nsanja ya Olonda,8/15/2014, ptsa. 29-306/1/1987, ptsa. 30-31
35 Koma amene aonedwa kuti ndi oyenerera kudzapeza moyo pa nthawi imeneyo nʼkudzaukitsidwa kwa akufa sadzakwatira kapena kukwatiwa.+