Luka 20:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Iwo amalanda chuma cha akazi* amasiye ndipo amapereka mapemphero ataliatali pofuna kudzionetsera.* Anthu amenewa adzalandira chilango chowawa kwambiri.”* Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:47 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 17
47 Iwo amalanda chuma cha akazi* amasiye ndipo amapereka mapemphero ataliatali pofuna kudzionetsera.* Anthu amenewa adzalandira chilango chowawa kwambiri.”*