Luka 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 iye ananena kuti: “Kunena za zinthu zimene mukuzionazi, masiku adzafika pamene sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:6 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 3
6 iye ananena kuti: “Kunena za zinthu zimene mukuzionazi, masiku adzafika pamene sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+