Luka 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anayankha kuti: “Samalani kuti asadzakusocheretseni,+ chifukwa ambiri adzabwera mʼdzina langa nʼkumanena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ komanso adzanena kuti, ‘Nthawi ija yayandikira.’ Musadzawatsatire.+
8 Iye anayankha kuti: “Samalani kuti asadzakusocheretseni,+ chifukwa ambiri adzabwera mʼdzina langa nʼkumanena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ komanso adzanena kuti, ‘Nthawi ija yayandikira.’ Musadzawatsatire.+