-
Luka 21:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Anthu adzakomoka chifukwa cha mantha komanso chifukwa choyembekezera zimene zichitikire dziko lapansi kumene kuli anthu, popeza mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka.
-