Luka 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa, chimene chinkadziwikanso kuti Pasika,+ chinali chitayandikira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 266 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 8
22 Tsopano Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa, chimene chinkadziwikanso kuti Pasika,+ chinali chitayandikira.+