-
Luka 22:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndipo mukauze mwininyumba imeneyo kuti, ‘Mphunzitsi wanena kuti: “Chipinda cha alendo chili kuti mmene ine ndingadyeremo Pasika limodzi ndi ophunzira anga?”’
-