-
Luka 22:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho ananyamuka ndipo zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Ndipo anakonza zinthu zonse zofunika pa Pasika.
-