Luka 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa Mwana wa munthu achoka mogwirizana ndi zimene zinanenedweratu.+ Koma tsoka kwa munthu amene akumupereka!”+
22 Chifukwa Mwana wa munthu achoka mogwirizana ndi zimene zinanenedweratu.+ Koma tsoka kwa munthu amene akumupereka!”+