Luka 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho anayamba kukambirana pakati pawo za amene anakonza chiwembu chimenecho.+