Luka 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kodi wamkulu ndi ndani, amene akudya patebulo kapena amene akutumikira? Kodi si amene akudya patebulo? Koma ine ndili pakati panu ngati wotumikira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:27 Yesu—Ndi Njira, tsa. 272 Nsanja ya Olonda,3/15/2003, tsa. 57/15/1990, ptsa. 8-9
27 Kodi wamkulu ndi ndani, amene akudya patebulo kapena amene akutumikira? Kodi si amene akudya patebulo? Koma ine ndili pakati panu ngati wotumikira.+